Jeremiah 18:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Nyamuka, upite ku nyumba ya munthu woumba mbiya, kumeneko ukamva mau anga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tauka, tatsikira kunyumba ya woumba, pamenepo ndidzakumvetsa mau anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pita ku nyumba ya munthu wowumba mbiya, ndipo kumeneko ndikakuwuza mawu anga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tauka, tatsikira ku nyumba ya woumba, pamenepo ndidzakumvetsa mau anga.