Jeremiah 18:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero ndidatsikira ku nyumba ya woumba mbiya, ndipo ndidampeza akuumba mbiya pa mkombero.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinatsikira kunyumba ya woumba, ndipo, taonani, anaumba ntchito yake ndi njinga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho ndinatsikira ku nyumba ya wowumba mbiya, ndipo ndinamuona akuwumba mbiya pa mkombero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinatsikira ku nyumba ya woumba, ndipo, taonani, anaumba nchito yace ndi njinga.