Jeremiah 18:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati ndichenjeza mtundu wa anthu kapena ufumu kuti ndidzaugwetsa ndi kuuwononga,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mphindi imene ndidzanena za mtundu wa anthu, kapena za ufumu, kuti ndizule ndi kupasula ndi kuononga;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati nditalengeza kuti mtundu wina wa anthu kapena ufumu wina ndiwuzula, kuwugwetsa ndi kuwuwononga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mphindi imene ndidzanena za mtundu wa anthu, kapena za ufumu, kuti ndizule ndi kupasula ndi kuononga;