Jeremiah 18:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ngati mtundu umene ndauchenjezawo uleka machimo ake, ndiye kuti sindidzaulanga monga m'mene ndinkaganizira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ngati mtundu umene, ndaunenera, udzatembenuka kuleka choipa chao, ndidzaleka choipacho ndidati ndiwachitire.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo ngati mtundu wa anthu umene ndawuchenjezawo ulapa zoyipa zawo, ndiye kuti Ine ndidzaleka ndipo sindidzabweretsa pa anthuwo mavuto amene ndinakonzekera kuwachitira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ngati mtundu umene, ndaunenera, udzatembenuka kuleka coipa cao, ndidzaleka coipaco ndidati ndiwacitire.