Jeremiah 18:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Momwemonso ngati ndifuna kuyambitsa ndi kukhazikitsa mtundu kapena ufumu wina,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mphindi imene ndikanenera mtundu, ndi ufumu, kuti ndimangitse mudzi wake ndi kuuoka;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ngati ndilengeza kuti ndikufuna kumanga ndi kukhazikitsa mtundu wa anthu kapena ufumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mphindi imene ndikanenera mtundu, ndi ufumu, kuti ndimangitse mudzi wace ndi kuuoka;