Jeremiah 19:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adandiwuza kuti, “Pita ukagule mtsuko wadothi kwa munthu woumba. Utenge akuluakulu ena, ndiponso ansembe ena okhwimapo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atero Yehova, Pita, nugule nsupa ya woumba, nutenge akulu a anthu, ndi akulu a ansembe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anandiwuza kuti, “Pita ukagule mʼphika wadothi kwa munthu wowumba. Utenge akuluakulu ena a anthuwa ndi ansembe
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atero Yehova, Pita, nugule nsupa ya woumba, nutenge akuru a anthu, ndi akuru a ansembe;