Jeremiah 19:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Umu ndimo m'mene ndidzaŵachitire malo ano pamodzi ndi anthu ake omwe. Mzindawu ndidzausandutsa ngati Tofeti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzatero ndi malo ano, ati Yehova, ndi okhalamo, kusanduliza mudzi uwu ngati Tofeti;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Umu ndi mmene ndidzachitire ndi malo ano pamodzi ndi anthu okhalamo, akutero Yehova. Ndidzasandutsa mzindawu kukhala ngati Tofeti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzatero ndi malo ano, ati Yehova, ndi okhalamo, kusanduliza mudzi uwu ngati Tofeti;