Jeremiah 2:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pitani chakuzambwe, ku chilumba cha Kitimu, mukaone, tumani anthu chakuvuma, ku Kedara, akafufuze. Mudzaona kuti zoterezi sizidachitikepo nkale lonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti pitani ku zisumbu za Kitimu nimuone; tumizani ku Kedara nimulingalire bwino; nimuone ngati chinalipo chotere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pitani kumadzulo ku chilumba cha Kitimu, ndipo mukaone, tumizani anthu ku Kedara kuti akafufuze bwino; ndipo muona kuti zinthu zoterezi sizinachitikepo nʼkale lomwe:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti pitani ku zisumbu za Kitimu nimuone; tumizani ku Kedara nimulingalire bwino; nimuone ngati cinalipo cotere.