Jeremiah 2:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ulipo mtundu wa anthu uliwonse umene udasinthapo milungu yake, ngakhale kuti si milungu konse? Komabe anthu anga asinthitsa Mulungu wao waulemerero ndi milungu yachabechabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi mtundu wa anthu unasintha milungu yao, imene siili milungu? Koma anthu anga anasintha ulemerero wao ndi chosapindula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ulipo mtundu wa anthu uliwonse umene unasinthapo milungu yake? (Ngakhale kuti si milungu nʼkomwe). Koma anthu anga asinthitsa Mulungu wawo waulemerero ndi mafano achabechabe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi mtundu wa anthu unasintha milungu yao, imene siiri milungu? Koma anthu anga anasintha ulemerero wao ndi cosapindula.