Jeremiah 2:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi zakuwonekerani chifukwa mudasiya Chauta, Mulungu wanu, pamene Iye adakuikani pa njira yabwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi sunadzichitira ichi iwe wekha popeza unasiya Yehova Mulungu wako, pamene anatsogolera iwe panjira?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zimenezitu zakuchitikirani chifukwa munasiya Yehova Mulungu wanu pamene Iye ankakutsogolerani pa njira yanu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi sunadzicitira ici iwe wekha popeza unasiya Yehova Mulungu wako, pamene anatsogolera iwe panjira?