Jeremiah 2:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe ndidaakuwoka iwe Israele ngati mtengo wa mphesa wosankhidwa, udaali mpesa wabwino kwambiri. Nanga wasanduka bwanji mpesa wachabechabe, wonga wakutchire?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Ine ndinakuoka mpesa wangwiro, mbeu yoona; kodi bwanji wandisandukira Ine mbeu yopanda pake, ya mpesa wachilendo?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndinakudzala iwe ngati mtengo wampesa wosankhika; unali mpesa wabwino kwambiri ndi wodalirika. Nanga nʼchifukwa chiyani wasanduka mpesa wachabechabe wonga wa kutchire?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Ine ndinakuoka mpesa wangwiro, mbeu yoona; kodi bwanji wandisandukira Ine mbeu yopanda pace, ya mpesa wacilendo?