Jeremiah 2:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuti, “Kodi mukundiimbiranji mlandu? Nonsenu mwandipandukira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chanji mudzatsutsana ndi Ine nonse? Mwandilakwira Ine, ati Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi mukundizengeranji mlandu? Nonse mwandiwukira,” akutero Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa canji mudzatsutsana ndi Ine nonse? mwandilakwira Ine, ati Yehova.