Jeremiah 2:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidalanga ana anu popanda phindu, sadaphunzirepo nkanthu komwe. Monga mkango wolusa mudapha aneneri anu ndi lupanga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndapanda ana anu mwachabe; sanamvere kulanga; lupanga lanu ladya aneneri anu, monga mkango wakuononga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ine ndinalanga anthu ako popanda phindu; iwo sanaphunzirepo kanthu. Monga mkango wolusa, lupanga lanu lapha aneneri anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndapanda ana anu mwacabe; sanamvera kulanga; lupanga lanu ladya aneneri anu, monga mkango wakuononga.