Jeremiah 2:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mumadziŵa bwino njira zopezera zibwenzi zam'seri. Ngakhale akazi oipa kwambiri omwe mumaŵaphunzitsa ndinu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi sukonzadi njira yako kufunafuna chilakolako? Chifukwa chake waphunzitsa akazi oipa njira zako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mumadziwa bwino njira zopezera zibwenzi! Choncho ngakhale akazi oyipa omwe mumawaphunzitsa njira zanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi sukonzadi njira yako kufunafuna cilakolako? cifukwa cace waphunzitsa akazi oipa njira zako.