Jeremiah 2:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
inu mukunena kuti, ‘Ndife osalakwa, mkwiyo wa Chauta wapola tsopano!’ Ine ndidzakuimbanibe mlandu chifukwa chonena kuti simudachimwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma unati, Ndili wosachimwa ndithu; mkwiyo wake wachoka pa ine. Taona, ndidzakuweruza iwe, chifukwa uti, Sindinachimwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
inu mukunena kuti, ‘Ndife osalakwa, sadzatikwiyira.’ Ndidzakuyimbani mlandu chifukwa mukunena kuti, ‘Ife sitinachimwe.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma unati, Ndiri wosacimwa ndithu; mkwiyo wace wacoka pa ine. Taona, ndidzakuweruza iwe, cifukwa uti, Sindinacimwa.