Jeremiah 2:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bwanji mukudzipeputsa nokha posinthasintha njira zanu! Ejipito adzakugwiritsani mwala monga muja adakuchititsirani manyazi Aasiriya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Bwanji uyendayenda kwambiri ndi kusintha njira yako? Udzachitanso manyazi ndi Ejipito monga unachita manyazi ndi Asiriya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chiyani mukunkabe nimusinthasintha njira zanu? Aigupto adzakukhumudwitsani monga momwe Asiriya anakuchititsani manyazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Bwanji uyendayenda kwambiri ndi kusintha njira yako? udzacitanso manyazi ndi Aigupto monga unacita manyazi ndi Asuri.