Jeremiah 2:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu zidzukulu za Yakobe, mabanja onse a Israele, mverani mau a Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tamvani mau a Yehova, iwe nyumba ya Yakobo, ndi inu mabanja onse a nyumba ya Israele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Imvani mawu a Yehova, inu zidzukulu za Yakobo, inu mafuko onse a Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tamvani mau a Yehova, iwe nyumba ya Yakobo, ndi inu mabanja onse a nyumba ya Israyeli;