Jeremiah 20:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
chifukwa choti sadandiphere m'mimba, kuti mai wanga asanduke manda anga, ndipo kuti mimba yake ikhale chitupire.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa sanandiphe ine m'mimba; kuti mai wanga akhale manda anga, ndi mimba yake yaikulu nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa sanandiphere mʼmimba, kuti amayi anga asanduke manda anga, mimba yawo ikhale yayikulu mpaka kalekale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa sanandipha ine m'mimba; kuti mai wanga akhale manda anga, ndi mimba yace yaikuru nthawi zonse.