Jeremiah 20:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi chifukwa chiyani ndidabadwa? Kodi ndidabadwira mavuto ndi chisoni, kuti moyo wanga ukhale wa manyazi okhaokha?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chanji ndinatuluka m'mimba kuti ndione kutopa ndi kulira, kuti masiku anga athe ndi manyazi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndinabadwira mavuto ndi chisoni kuti moyo wanga ukhale wamanyazi wokhawokha?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa canji ndinaturuka m'mimba kuti ndione kutopa ndi kulira, kuti masiku anga athe ndi manyazi?