Jeremiah 20:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikamalankhula, ndimakweza mau, ndimafuula kuti, “Ndeu kuno, taonongeka!” Mau anu, Inu Chauta, andisandutsa wonyozeka ndi wonyodoledwa masiku onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti paliponse ndinena, ndifuula; ndifuula, Chiwawa ndi chofunkha; pakuti mau a Yehova ayesedwa kwa ine chitonzo, ndi choseketsa, dzuwa lonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi iliyonse ndikamayankhula, ndimafuwula kunena kuti, ziwawa kuno! Tikuwonongeka! Mawu anu Yehova andisandutsa chinthu chonyozeka ndipo ndimachitidwa chipongwe tsiku lonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti pali ponse ndinena, ndipfuula; ndipfuula, Ciwawa ndi cofunkha; pakuti mau a Mulungu ayesedwa kwa ine citonzo, ndi coseketsa, dzuwa lonse.