Jeremiah 21:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zedekiya, mfumu ya ku Yuda, adatuma Pasuri mwana wa Malakiya, ndiponso wansembe Zefaniya mwana wa Maseiya, naŵauza kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau amene anadza kwa Yeremiya kuchokera kwa Yehova, pamene Zedekiya mfumu anatuma kwa iye Pasuri mwana wa Malikiya, ndi Zefaniya mwana wake wa Maaseiya wansembe, akati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu Zedekiya inatuma Pasuri mwana wa Malikiya ndi wansembe Zefaniya mwana wa Maseya kwa Yeremiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, pamene Zedekiya mfumu anatuma kwa iye Pasuri mwana wa Malikiya, ndi Zefaniya mwana wace wa Maseya wansembe, akati,