Jeremiah 21:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakulangani potsata ntchito zanu. Ndidzatentha nkhalango yanu, moto udzapsereza zonse zimene zakuzungulirani,” akuterotu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzakulangani inu monga mwa chipatso cha ntchito zanu, ati Yehova; ndipo ndidzayatsa moto m'nkhalango mwake, ndipo udzatha zonse zomzungulira iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakulangani molingana ndi ntchito zanu, akutero Yehova. Ndidzatentha nkhalango zanu; moto udzapsereza zonse zimene zakuzungulirani.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzakulangani inu monga mwa cipatso ca nchito zanu, ati Yehova; ndipo ndidzayatsa moto m'nkhalango mwace, ndipo udzatha zonse zomzungulira iye.