Jeremiah 21:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akunena kuti, “Anthu ameneŵa udzaŵauzenso kuti asankhulepo: kodi afuna moyo kapena imfa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo uziti kwa anthu awa, Yehova atero, Taonani, ndaika pamaso panu njira ya moyo ndi njira ya imfa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yehova anati ndiwawuzenso anthu amenewa kuti asankhe pakati pa moyo ndi imfa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo uziti kwa anthu awa, Yehova atero, Taonani, ndaika pamaso panu njira ya moyo ndi njira ya imfa.