Jeremiah 22:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngati sudzamvera mau anga, ndikulumbira pali Ine ndemwe, kuti nyumba imeneyi idzasanduka bwinja!’ ” Akuterotu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati simudzamva mau amenewa, Ine ndilumbira, pali Ine mwini, ati Yehova, nyumba iyi idzakhala yabwinja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati sumvera malamulo awa, akutero Yehova, ndikulumbira pali Ine ndemwe kuti nyumba ino yaufumu idzasanduka bwinja.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati simudzamva mau amenewa, Ine ndilumbira, pali Ine mwini, ati Yehova, nyumba iyi idzakhala yabwinja.