Jeremiah 23:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsoka kwa abusa amene amaononga ndi kumwaza nkhosa za pabusa panga,” akutero Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsoka abusa amene athetsa nabalalitsa nkhosa za busa langa! Ati Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsoka kwa abusa amene akuwononga ndi kubalalitsa nkhosa za pabusa panga!” akutero Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsoka abusa amene athetsa nabalalitsa nkhosa za busa langa! ati Yehova.