Jeremiah 23:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndidati, “Mwa aneneriwo ndani amene adakhala nao m'bungwe la Chauta? Ndani adamuwona ndi kumva mau ake? Ndani mwa iwo adasamalako mau ake ndi kuŵamvera?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndani waima m'upo wa Yehova, kuti aone namve mau ake? Ndani wazindikira mau anga, nawamva?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndikuti, “Koma ndani wa iwo amene anakhalapo mu msonkhano wa Yehova? Ndani anaonapo kapena kumvapo mawu ake? Ndani mwa iwo analabadirako za mawu ake ndi kuwamvera?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndani waima m'upo wa Yehova, kuti aone namve mau ace? ndani wazindikira mau anga, nawamva?