Jeremiah 23:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkwiyo wa Chauta sudzaleka, mpaka atachita zonse zimene adatsimikiza mumtima mwake. Zimenezi mudzazidziŵa masiku akubweraŵa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mkwiyo wa Yehova sudzabwerera, mpaka atachita, mpaka atatha maganizo a mtima wake; masiku otsiriza mudzachidziwa bwino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkwiyo wa Yehova sudzaleka mpaka atachita zonse zimene anatsimikiza mu mtima mwake. Mudzazizindikira bwino zimenezi masiku akubwerawa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mkwiyo wa Yehova sudzabwerera, mpaka atacita, mpaka atatha maganizo a mtima wace; masiku otsiriza mudzacidziwa bwino.