Jeremiah 23:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi zabodzazi adzazisunga mumtima mwao mpaka liti aneneri onamaŵa, amene amalosa zonyenga za mumtima mwao?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ichi chidzakhala masiku angati m'mtima mwa aneneri amene anenera zonama; ndiwo aneneri a chinyengo cha mtima wao?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi zabodzazi zidzakhalabe mʼmitima ya aneneriwa mpaka liti? Iwotu amalosera zonyenga za mʼmitima yawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ici cidzakhala masiku angati m'mtima mwa aneneri amene anenera zonama; ndiwo aneneri a cinyengo ca mtima wao?