Jeremiah 23:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikuŵatsutsa aneneri amene amakonda kulankhula zamabodza, namanena kuti, ‘Ameneŵa ndiwo mau a Chauta.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, Ine ndidana ndi aneneri, ati Yehova, amene achita ndi malilime ao, ndi kuti, Ati Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akuti, “Inde, Ine ndikudana ndi aneneri amene amakonda kuyankhula zabodza nʼkumanena kuti, ‘Amenewa ndi mawu a Yehova.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, Ine ndidana ndi aneneri, ati Yehova, amene acita ndi malilime ao, ndi kuti, Ati Iye.