Jeremiah 23:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo mneneri, wansembe, kapena munthu wina aliyense, wonena kuti, ‘Nawu uthenga wolemetsa wa Chauta,’ ameneyo ndidzamulanga pamodzi ndi banja lake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma za mneneri, ndi wansembe, ndi anthu, amene adzati, Katundu wa Yehova, ndidzamlanga munthuyo ndi nyumba yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati mneneri kapena wansembe kapenanso munthu wina aliyense anena kuti, ‘Uthenga wolemetsa wa Yehova ndi uwu,’ Ine ndidzalanga munthu ameneyo pamodzi ndi banja lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma za mneneri, ndi wansembe, ndi anthu, amene adzati, Katundu wa Yehova, ndidzamlanga munthuyo ndi nyumba yace.