Jeremiah 23:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mau amene aliyense azifunsa mnzake kapena mbale wake akhale akuti, ‘Kodi Chauta wanena zotani?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzatero yense kwa mnansi wake, ndi yense kwa mbale wake, Yehova wayankha chiyani? Ndipo Yehova wanena chiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma chimene aliyense wa inu azifunsa kwa mnzake kapena mʼbale wake ndi ichi: ‘Kodi Yehova wayankha chiyani?’ kapena ‘Yehova wayankhula chiyani?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzatero yense kwa mnansi wace, ndi yense kwa mbale wace, Yehova wayankha ciani? ndipo Yehova wanena ciani?