Jeremiah 23:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono iwe Yeremiya udzamufunse mneneri kuti, ‘Kodi Chauta wayankha zotani?’ Kapena kuti, ‘Kodi Chauta wanena zotani?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Uzitero kwa mneneri, Yehova wakuyankha chiyani? Ndipo Yehova wanenanji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono iwe Yeremiya udzamufunse mneneri kuti, ‘Kodi Yehova wakuyankha chiyani?’ kapena, ‘Kodi Yehova wayankhula chiyani?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Uzitero kwa mneneri, Yehova wakuyankha ciani? ndipo Yehova wanenanji?