Jeremiah 23:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngati munena kuti, ‘Nawu uthenga wolemetsa wa Chauta,’ Chautayo akuti, ‘Popeza kuti mwanena mau akuti nawu uthenga wolemetsa wa Chauta, pamene ndidakuuzani kuti musanene mau ameneŵa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati muti, Katundu wa Yehova, chifukwa chake Yehova atero: Chifukwa muti mau awa, Katundu wa Yehova, ndipo ndatuma kwa inu, kuti, Musati, Katundu wa Yehova;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati mudzanena kuti, ‘Nawu uthenga wolemetsa wa Yehova,’ ndiye tsono Yehova akuti, ‘Popeza mwagwiritsa ntchito mawu akuti: Nawu uthenga wolemetsa wa Yehova, mawu amene ndinakuletsani kuti musawatchule,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati muti, Katundu wa Yehova, cifukwa cace Yehova atero: Cifukwa muti mau awa, Katundu wa Yehova, ndipo ndatuma kwa inu, kuti, Musati, Katundu wa Yehova;