Jeremiah 23:40 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakunyozani mpaka muyaya, ndikakuchititsani manyazi osaiŵalika.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ndidzakutengerani inu chitonzo chamuyaya, ndi manyazi amuyaya, amene sadzawailika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakunyozani mpaka muyaya. Ndidzakuchititsani manyazi osayiwalika.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ndidzakutengerani inu citonzo camuyaya, ndi manyazi amuyaya, amene sadzaiwalika.