Jeremiah 24:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzaŵapha ndi nkhondo, njala ndi mliri, mpaka onsewo nditaŵapululiratu m'dziko limene ndidaŵapatsa iwowo ndi makolo ao.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzatuma lupanga, ndi njala, ndi chaola mwa iwo, mpaka athedwa m'dziko limene ndinapatsa iwo ndi makolo ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzawatumizira nkhondo, njala ndi mliri mpaka atawonongedwa mʼdziko limene ndinawapatsa iwo ndi makolo awo.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzatuma lupanga, ndi njala, ndi caola mwa iwo, mpaka athedwa m'dziko limene ndinapatsa iwo ndi makolo ao.