Jeremiah 25:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzathetsa chimwemwe chonse ndi kusangalala konse pakati pao. Ndidzaletseratu mau achikondwerero a mkwati wamwamuna ndi mkwati wamkazi. Sikudzamvekanso phokoso la mphero, ndipo ndidzazima nyale zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiponso ndidzawachotsera mau akusekera ndi mau akukondwera, ndi mau a mkwati, ndi mau a mkwatibwi, mau a mphero, ndi kuwala kwa nyali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzathetsa mfuwu wachimwemwe ndi wachisangalalo, mawu a mkwati ndi mkwatibwi, phokoso la mphero ndi kuwala kwa nyale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiponso ndidzawacotsera mau akusekera ndi mau akukondwera, ndi mau a mkwati, ndi mau a mkwatibwi, mau a mphero, ndi kuwala kwa nyali.