Jeremiah 25:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adzakhala akapolo a anthu a mitundu yochuluka ndi a mafumu otchuka. Motero ndidzaŵabwezera potsata zochita zao ndi ntchito za manja ao.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mitundu yambiri ndi mafumu akulu adzayesa iwo atumiki ao; ndipo ndidzabwezera iwo monga mwa machitidwe ao, monga mwa ntchito ya manja ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo eni adzakhala akapolo a anthu a mitundu yochuluka ndi mafumu amphamvu. Ndidzawabwezera molingana ndi zochita zawo ndi ntchito za manja awo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mitundu yambiri ndi mafumu akuru adzayesa iwo atumiki ao; ndipo ndidzabwezera iwo monga mwa macitidwe ao, monga mwa nchito ya manja ao.