Jeremiah 25:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atamwa, adzayamba kudzandira ndipo adzachita misala chifukwa cha nkhondo imene ndikutumiza pakati pao.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzamwa, nadzayenda dzandidzandi, nadzachita misala, chifukwa cha lupanga limene Ine ndidzatumiza mwa iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akadzamwa adzayamba kudzandira ndi kuchita misala chifukwa cha nkhondo imene ndikuyitumiza pakati pawo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzamwa, nadzayenda dzandi dzandi, nadzacita misala, cifukwa ca lupanga limene Ine ndidzatumiza mwa iwo.