Jeremiah 25:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ndidalandira chikhocho kumanja kwa Chauta ndipo ndidapatsa anthu a mitundu yonse, kuti amwe monga momwe Chauta adaandilamulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinatenga chikho pa dzanja la Yehova, ndinamwetsa mitundu yonse, imene Yehova ananditumizirako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho ine ndinatenga chikhocho mʼdzanja la Yehova ndipo ndinamwetsa mitundu yonse ya anthu kumene Iye ananditumako:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinatenga cikho pa dzanja la Yehova, ndinamwetsa mitundu yonse, imene Yehova ananditumizirako;