Jeremiah 25:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adanditumanso kwa Farao, mfumu ya ku Ejipito, kwa nduna zake, kwa akalonga ake, kwa anthu ake onse,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Farao mfumu ya ku Ejipito, ndi atumiki ake, ndi akulu ake, ndi anthu ake onse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ananditumanso kwa Farao, mfumu ya ku Igupto, kwa atumiki ake, nduna zake ndi kwa anthu ake onse,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Farao mfumu ya ku Aigupto, ndi atumiki ace, ndi akuru ace, ndi anthu ace onse;