Jeremiah 25:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mneneri Yeremiya adauza anthu onse a ku Yuda ndi onse okhala ku Yerusalemu kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene mneneri Yeremiya ananena kwa anthu onse a Yuda, ndi onse okhala m'Yerusalemu, kuti:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho mneneri Yeremiya anawuza anthu onse a ku Yuda pamodzi ndi onse amene amakhala mu Yerusalemu kuti:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amene Yeremiya ananena kwa anthu onse a Yuda, ndi onse okhala m'Yerusalemu, kuti: