Jeremiah 25:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndi kwa anthu a mitundu ina yachilendo yokhala pakati pao. Adanditumanso kwa mafumu onse a ku dziko la Uzi, kwa mafumu onse a Afilisti, ndiye kuti ku Asikeloni, ku Gaza, ku Ekeroni ndi ku chigawo chotsala cha ku Asidodi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi anthu onse osanganizidwa, ndi mafumu onse a dziko la Uzi, ndi mafumu onse a dziko la Afilisti, ndi Asikeloni, ndi Gaza, ndi Ekeroni, ndi otsala a Asidodi,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi kwa anthu ena onse a mitundu yachilendo; mafumu onse a ku Uzi; mafumu onse a Afilisti, a ku Asikeloni, ku Gaza, ku Ekroni ndiponso kwa anthu a ku chigwa chotsala cha Asidodi;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi anthu onse osanganizidwa, ndi mafumu onse a dziko la Uzi, ndi mafumu onse a dziko la Afilisti, ndi Asikeloni, ndi Gaza, ndi Ekroni, ndi otsala a Asdodi,