Jeremiah 25:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adandituma kwa mafumu onse a ku Tiro ndi Sidoni, ndiponso kwa mafumu a maiko a m'mbali mwa nyanja, ndiye kuti
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi mafumu onse a Tiro, ndi mafumu onse a Sidoni, ndi mafumu a chisumbu chimene chili patsidya pa nyanja;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ananditumanso kwa mafumu onse a ku Turo ndi ku Sidoni; kwa mafumu a kutsidya la nyanja;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi mafumu onse a Turo, ndi mafumu onse a Zidoni, ndi mafumu a cisumbu cimene ciri patsidya pa nyanja;