Jeremiah 25:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adanditumanso kwa mafumu onse a ku Arabiya ndi kwa ena aja okhala m'chipululu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi amfumu onse a Arabiya, ndi mafumu onse a anthu osanganizidwa okhala m'chipululu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ananditumanso kwa mafumu onse a ku Arabiya ndi mafumu onse a anthu achilendo amene amakhala mʼchipululu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi mafumu onse a Arabiya, ndi mafumu onse a anthu osanganizidwa okhala m'cipululu;