Jeremiah 25:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mverani, abusa akulira, eniake a nkhosa akulira kwambiri, pakuti Chauta akuwononga busa lao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau akufuula abusa, ndi kukuwa mkulu wa zoweta! Pakuti Yehova asakaza busa lao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Imvani kulira kwa abusa, atsogoleri a nkhosa akulira, chifukwa Yehova akuwononga msipu wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau akupfuula abusa, ndi kukuwa mkuru wa zoweta! pakuti Yehova asakaza busa lao.