Jeremiah 25:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta waŵasiya anthu ake ngati mkango wosiya phanga lake, ndipo dziko lao lasanduka chipululu, chifukwa cha mazunzo a nkhondo ndi mkwiyo woopsa wa Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wasiya ngaka yake, monga mkango; pakuti dziko lao lasanduka chizizwitso chifukwa cha ukali wa lupanga losautsa, ndi chifukwa cha mkwiyo wake waukali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati mkango, Yehova wasiya phanga lake, pakuti dziko lawo lasanduka chipululu chifukwa cha nkhondo ya owazunza ndiponso chifukwa cha mkwiyo woopsa wa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wasiya ngaka yace, monga mkango; pakuti dziko lao lasanduka cizizwitso cifukwa ca ukali wa lupanga losautsa, ndi cifukwa ca mkwiyo wace waukali.