Jeremiah 25:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musamatsate milungu ina, kumaitumikira ndi kumaipembedza. Musamapute mkwiyo wanga ndi mafano opanga ndi manja anu. Tsono Ine sindidzakuwonongani.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
musatsate milungu ina kuitumikira, ndi kuigwadira, musautse mkwiyo wanga ndi ntchito ya manja anu; ndingachitire inu choipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musatsatire milungu ina nʼkuyitumikira ndi kuyipembedza. Musapute mkwiyo wanga ndi mafano amene mwapanga ndi manja anu. Mukatero Ine sindidzakuwonongani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
musatsate milungu yina kuitumikira, ndi kuigwadira, musautse mkwiyo wanga ndi nchito ya manja anu; ndingacitire inu coipa.