Jeremiah 25:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Chauta Wamphamvuzonse akunena kuti, “Chifukwa choti simudamvere mau anga,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake Yehova wa makamu atero: Popeza simunamvera mau anga,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake Yehova Wamphamvuzonse akuti, “Chifukwa simunamvere mawu anga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace Yehova wa makamu atero: Popeza simunamvera mau anga,