Jeremiah 26:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Yehoyakimu, mwana wa Yosiya mfumu ya ku Yuda, adayamba kulamulira, Chauta adauza Yeremiya kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Poyamba kukhala mfumu Yehoyakimu mwana wake wa Yosiya, mfumu ya Yuda, panadza mau awa ochokera kwa Yehova, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehoyakimu, mwana wa Yosiya mfumu ya ku Yuda atayamba kulamulira, Yehova anayankhula ndi Yeremiya kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Poyamba kukhala mfumu Yehoyakimu mwana wace wa Yosiya, mfumu ya Yuda, panadza mau awa ocokera kwa Yehova, kuti,