Jeremiah 26:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akuluakulu ena am'dzikomo adaimiriranso nauza anthu onse amene adasonkhanawo kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anauka akulu ena a m'dziko, nati kwa msonkhano wa anthu, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akuluakulu ena a mʼdzikomo anayimirira ndi kuwuza gulu lonse la anthu kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anauka akuru ena a m'dziko, nati kwa msonkhano wa anthu, kuti,